Akolose 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse. Pitirizani kuphunzitsana ndi kulimbikitsana* ndi masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu komanso nyimbo zauzimu zoyamikira. Pitirizani kuimbira Yehova* mʼmitima yanu.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2023, tsa. 32 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 10 Nsanja ya Olonda,5/1/1994, ptsa. 11-12
16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse. Pitirizani kuphunzitsana ndi kulimbikitsana* ndi masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu komanso nyimbo zauzimu zoyamikira. Pitirizani kuimbira Yehova* mʼmitima yanu.+
3:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2023, tsa. 32 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 10 Nsanja ya Olonda,5/1/1994, ptsa. 11-12