Akolose 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 chifukwa mukudziwa kuti mphoto imene mudzalandire ndi cholowa chochokera kwa Yehova.*+ Tumikirani Ambuye wanu Khristu monga akapolo. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:24 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 37 Nsanja ya Olonda,6/15/1997, tsa. 32
24 chifukwa mukudziwa kuti mphoto imene mudzalandire ndi cholowa chochokera kwa Yehova.*+ Tumikirani Ambuye wanu Khristu monga akapolo.