Akolose 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu amene ndinu ambuye, muzichitira akapolo anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, chifukwa mukudziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+
4 Inu anthu amene ndinu ambuye, muzichitira akapolo anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, chifukwa mukudziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+