-
Akolose 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ndi Yesu, amene amadziwikanso kuti Yusito, akuti moni. Iwowa ali mʼgulu la anthu odulidwa. Amenewa okha ndi antchito anzanga pa zinthu zokhudzana ndi Ufumu wa Mulungu ndipo amandilimbikitsa kwambiri.
-