Akolose 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse kuti mupitirize kukhala olimba mwauzimu komanso kuti musamakayikire ngakhale pangʼono zinthu zonse zimene Mulungu adzachite. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 Nsanja ya Olonda,2/15/2008, ptsa. 3-412/15/2000, ptsa. 15-16, 19-245/15/1997, tsa. 31
12 Epafura,+ amene anachokera pakati panu, kapolo wa Khristu Yesu, akuti moni. Iye amakupemphererani mwakhama nthawi zonse kuti mupitirize kukhala olimba mwauzimu komanso kuti musamakayikire ngakhale pangʼono zinthu zonse zimene Mulungu adzachite.