Akolose 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ kumpingo wa Alaodikaya, ndiponso kuti inuyo muwerenge yochokera ku Laodikaya. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,8/15/2008, tsa. 2811/15/1990, tsa. 26
16 Kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ kumpingo wa Alaodikaya, ndiponso kuti inuyo muwerenge yochokera ku Laodikaya.