Akolose 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo amene andimanga nawo kundende kuno.+ Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.
18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo amene andimanga nawo kundende kuno.+ Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.