1 Atesalonika 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipotu mukudziwa kuti sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo, kapena kuchita zachiphamaso ndi zolinga zadyera.+ Mulungu ndi mboni yathu.
5 Ndipotu mukudziwa kuti sitinayambe talankhulapo mawu okuyamikirani mwachinyengo, kapena kuchita zachiphamaso ndi zolinga zadyera.+ Mulungu ndi mboni yathu.