-
1 Atesalonika 2:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Pamene tinali ndi inu okhulupirira, tinali okhulupirika, tinkachita zinthu zachilungamo ndiponso tinalibe chifukwa chotinenezera. Inuyo komanso Mulungu ndinu mboni zathu.
-