1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tinkachita zimenezi nʼcholinga choti mupitirize kuyenda mʼnjira imene Mulungu amafuna.+ Iye ndi amene akukuitanani kuti mulowe mu Ufumu wake+ ndi kulandira ulemerero.+
12 Tinkachita zimenezi nʼcholinga choti mupitirize kuyenda mʼnjira imene Mulungu amafuna.+ Iye ndi amene akukuitanani kuti mulowe mu Ufumu wake+ ndi kulandira ulemerero.+