1 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo akuchita zimenezi pamene akuyesa kutiletsa kulalikira kwa anthu a mitundu ina zimene angachite kuti adzapulumuke.+ Pochita zimenezi, nthawi zonse akuwonjezera machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+
16 Iwo akuchita zimenezi pamene akuyesa kutiletsa kulalikira kwa anthu a mitundu ina zimene angachite kuti adzapulumuke.+ Pochita zimenezi, nthawi zonse akuwonjezera machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+