1 Atesalonika 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho pamene sitinathenso kupirira, tinaona kuti ndi bwino kuti tipitirize kukhala ku Atene.+