1 Atesalonika 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tinachita zimenezi kuti pasapezeke aliyense amene chikhulupiriro chake chafooka* ndi masautso amenewa. Chifukwa inunso mukudziwa kuti sitingapewe kukumana ndi mavuto ngati amenewa.*+
3 Tinachita zimenezi kuti pasapezeke aliyense amene chikhulupiriro chake chafooka* ndi masautso amenewa. Chifukwa inunso mukudziwa kuti sitingapewe kukumana ndi mavuto ngati amenewa.*+