-
1 Atesalonika 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndipotu mukuchita kale zimenezi kwa abale onse ku Makedoniya konse. Koma tikukulimbikitsani abale kuti mupitirize kuchita zimenezi kuposa mmene mukuchitira.
-