1 Atesalonika 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu wamtendereyo akupatuleni kuti muchite utumiki wake. Ndipo pa mbali zonse abale, mzimu wanu, moyo wanu komanso thupi lanu, zikhale zopanda chilema kapena cholakwa chilichonse, pa nthawi ya kukhalapo kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+ 1 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:23 Nsanja ya Olonda,9/15/2008, tsa. 295/1/1993, tsa. 11
23 Mulungu wamtendereyo akupatuleni kuti muchite utumiki wake. Ndipo pa mbali zonse abale, mzimu wanu, moyo wanu komanso thupi lanu, zikhale zopanda chilema kapena cholakwa chilichonse, pa nthawi ya kukhalapo kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+