2 Atesalonika 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo ndili limodzi ndi Silivano* komanso Timoteyo+ ndipo ndikulembera mpingo wa Atesalonika, womwe ndi wogwirizana ndi Mulungu Atate wathu komanso Ambuye Yesu Khristu kuti:
1 Ine Paulo ndili limodzi ndi Silivano* komanso Timoteyo+ ndipo ndikulembera mpingo wa Atesalonika, womwe ndi wogwirizana ndi Mulungu Atate wathu komanso Ambuye Yesu Khristu kuti: