-
2 Atesalonika 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Timakupemphererani kuti dzina la Ambuye wathu Yesu lilemekezeke mwa inu komanso kuti inu mulemekezeke mwa iye, mogwirizana ndi kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu ndi kwa Ambuye Yesu Khristu.
-