2 Atesalonika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa tikumva kuti ena akuyenda mosalongosoka pakati panu,+ sakugwira ntchito nʼkomwe, koma akulowerera nkhani zimene sizikuwakhudza.+
11 Chifukwa tikumva kuti ena akuyenda mosalongosoka pakati panu,+ sakugwira ntchito nʼkomwe, koma akulowerera nkhani zimene sizikuwakhudza.+