2 Atesalonika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu otero tikuwalamula ndi kuwachonderera mwa Ambuye Yesu Khristu kuti azigwira ntchito mwakhama popanda kulowerera nkhani za anthu ena ndipo azidya chakudya chimene iwowo achigwirira ntchito.+
12 Anthu otero tikuwalamula ndi kuwachonderera mwa Ambuye Yesu Khristu kuti azigwira ntchito mwakhama popanda kulowerera nkhani za anthu ena ndipo azidya chakudya chimene iwowo achigwirira ntchito.+