2 Atesalonika 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Ambuye wamtendere akupatseni mtendere nthawi zonse mʼnjira iliyonse.+ Ambuye akhale nanu nonsenu.
16 Tsopano Ambuye wamtendere akupatseni mtendere nthawi zonse mʼnjira iliyonse.+ Ambuye akhale nanu nonsenu.