2 Atesalonika 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Landirani moni wanga, amene ineyo Paulo ndalemba ndi dzanja langa.+ Nthawi zonse ndimalemba chonchi mʼmakalata anga onse, kuti mudziwe kuti ndine amene ndalemba. Umu ndi mmene ndimalembera.
17 Landirani moni wanga, amene ineyo Paulo ndalemba ndi dzanja langa.+ Nthawi zonse ndimalemba chonchi mʼmakalata anga onse, kuti mudziwe kuti ndine amene ndalemba. Umu ndi mmene ndimalembera.