1 Timoteyo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ndine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu molamulidwa ndi Mulungu amene ndi Mpulumutsi wathu komanso molamulidwa ndi Khristu Yesu, yemwe ndi chiyembekezo chathu.+
1 Ndine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu molamulidwa ndi Mulungu amene ndi Mpulumutsi wathu komanso molamulidwa ndi Khristu Yesu, yemwe ndi chiyembekezo chathu.+