-
1 Timoteyo 1:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Nditatsala pangʼono kupita ku Makedoniya, ndinakupempha kuti ukhalebe ku Efeso. Ndikukupemphanso kuti ukhalebe komweko nʼcholinga choti uletse anthu ena kuti asamaphunzitse zosiyana ndi zimene timaphunzitsa,
-