1 Timoteyo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndiponso kuti asamamvere nkhani zonama+ ndi zofufuzana mibadwo ya makolo.* Zimenezi nʼzosathandiza,+ koma zimangoyambitsa nkhani zopanda umboni ndipo siziphunzitsa anthu chilichonse chochokera kwa Mulungu chokhudza chikhulupiriro. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 16-184/1/1994, tsa. 30
4 ndiponso kuti asamamvere nkhani zonama+ ndi zofufuzana mibadwo ya makolo.* Zimenezi nʼzosathandiza,+ koma zimangoyambitsa nkhani zopanda umboni ndipo siziphunzitsa anthu chilichonse chochokera kwa Mulungu chokhudza chikhulupiriro.