1 Timoteyo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amenewa amafuna kukhala aphunzitsi+ a chilamulo koma samvetsa zimene akunena kapena mfundo zimene akuzilimbikira.
7 Anthu amenewa amafuna kukhala aphunzitsi+ a chilamulo koma samvetsa zimene akunena kapena mfundo zimene akuzilimbikira.