1 Timoteyo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipotu lamulo siliikidwa chifukwa cha munthu wolungama. Koma limaikidwa chifukwa cha anthu osamvera malamulo,+ oukira, osaopa Mulungu, ochimwa, osakhulupirika, onyoza zinthu zopatulika, opha abambo ndi amayi awo, opha anthu,
9 Ndipotu lamulo siliikidwa chifukwa cha munthu wolungama. Koma limaikidwa chifukwa cha anthu osamvera malamulo,+ oukira, osaopa Mulungu, ochimwa, osakhulupirika, onyoza zinthu zopatulika, opha abambo ndi amayi awo, opha anthu,