1 Timoteyo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, ndinachitiridwa chifundo kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire nʼcholinga choti adzapeze moyo wosatha.+
16 Komabe, ndinachitiridwa chifundo kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire nʼcholinga choti adzapeze moyo wosatha.+