1 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona, sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndiziphunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro ndi choonadi.
7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona, sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndiziphunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro ndi choonadi.