1 Timoteyo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ndikufuna kuti kulikonse amuna apitirize kupemphera. Azikweza manja mʼmwamba mokhulupirika kwa Mulungu,+ popanda kukwiya+ ndi kutsutsana.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,11/15/2002, tsa. 1911/15/1992, tsa. 23
8 Choncho, ndikufuna kuti kulikonse amuna apitirize kupemphera. Azikweza manja mʼmwamba mokhulupirika kwa Mulungu,+ popanda kukwiya+ ndi kutsutsana.+