1 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Asakhale woti wangobatizidwa kumene,*+ kuopera kuti angayambe kudzitukumula chifukwa cha kunyada nʼkulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Gulu, ptsa. 32, 34 Nsanja ya Olonda,9/1/1990, tsa. 26
6 Asakhale woti wangobatizidwa kumene,*+ kuopera kuti angayambe kudzitukumula chifukwa cha kunyada nʼkulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.