1 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nawonso akazi akhale opanda chibwana, ochita zinthu mosapitirira malire, okhulupirika pa zinthu zonse+ ndipo asakhale amiseche.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,10/15/1996, tsa. 17
11 Nawonso akazi akhale opanda chibwana, ochita zinthu mosapitirira malire, okhulupirika pa zinthu zonse+ ndipo asakhale amiseche.+