1 Timoteyo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti ngati ndingachedwe, udziwe zimene uyenera kuchita mʼnyumba ya Mulungu,+ imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo. Mpingowo ndi umene umalimbikitsa ndi kuteteza choonadi. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Nsanja ya Olonda,4/15/2007, tsa. 29
15 kuti ngati ndingachedwe, udziwe zimene uyenera kuchita mʼnyumba ya Mulungu,+ imene ndi mpingo wa Mulungu wamoyo. Mpingowo ndi umene umalimbikitsa ndi kuteteza choonadi.