1 Timoteyo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukamapereka malangizowa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino chimene wachitsatira mosamala.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, ptsa. 16-17 Utumiki wa Ufumu,1/2005, tsa. 1
6 Ukamapereka malangizowa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino chimene wachitsatira mosamala.+
4:6 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, ptsa. 16-17 Utumiki wa Ufumu,1/2005, tsa. 1