-
1 Timoteyo 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Usalole kuti munthu aliyense akuderere poona kuti ndiwe wamngʼono. Mʼmalomwake, ukhale chitsanzo kwa okhulupirika pa zimene umalankhula, makhalidwe ako, chikondi, chikhulupiriro ndi khalidwe loyera.
-