-
1 Timoteyo 5:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 ndipo akazi achikulire ngati amayi ako. Akazi achitsikana uzilankhula nawo ngati achemwali ako, ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse olakwika.
-