-
1 Timoteyo 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma usaike akazi amasiye achitsikana pamndandanda umenewu, chifukwa ngati atengeka ndi chilakolako chofuna mwamuna mʼmalo motumikira Khristu, amasankha kukwatiwa.
-