1 Timoteyo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso amangokhala osachita kanthu nʼkumangoyendayenda mʼmakomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakondanso miseche, kulowerera nkhani za eni+ komanso kulankhula zinthu zimene sayenera kulankhula. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, tsa. 186/15/2007, tsa. 2010/15/1989, ptsa. 11, 20 Galamukani!,7/8/1989, tsa. 20
13 Komanso amangokhala osachita kanthu nʼkumangoyendayenda mʼmakomo mwa anzawo. Kuwonjezera pa kumangokhala osachita kanthu, amakondanso miseche, kulowerera nkhani za eni+ komanso kulankhula zinthu zimene sayenera kulankhula.
5:13 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, tsa. 186/15/2007, tsa. 2010/15/1989, ptsa. 11, 20 Galamukani!,7/8/1989, tsa. 20