1 Timoteyo 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ndingakonde kuti akazi amasiye achitsikana azikwatiwa,+ kubereka ana+ ndiponso kusamalira banja nʼcholinga choti otsutsa asatipezere chifukwa. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:14 Nsanja ya Olonda,10/15/1989, tsa. 20
14 Choncho ndingakonde kuti akazi amasiye achitsikana azikwatiwa,+ kubereka ana+ ndiponso kusamalira banja nʼcholinga choti otsutsa asatipezere chifukwa.