1 Timoteyo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati mkazi aliyense wokhulupirira ali ndi achibale amene ndi akazi amasiye, iyeyo aziwathandiza, kuti akazi amasiyewo asachititse mpingo kupanikizika. Zikatero, mpingowo ungathe kuthandiza amene alidi akazi amasiye.*+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:16 Nsanja ya Olonda,8/1/1994, tsa. 28
16 Ngati mkazi aliyense wokhulupirira ali ndi achibale amene ndi akazi amasiye, iyeyo aziwathandiza, kuti akazi amasiyewo asachititse mpingo kupanikizika. Zikatero, mpingowo ungathe kuthandiza amene alidi akazi amasiye.*+