1 Timoteyo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Paja Mawu a Mulungu amati: “Usamange ngʼombe pakamwa pamene ikupuntha* mbewu.”+ Komanso amati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Nsanja ya Olonda,9/15/1989, tsa. 22
18 Paja Mawu a Mulungu amati: “Usamange ngʼombe pakamwa pamene ikupuntha* mbewu.”+ Komanso amati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+