1 Timoteyo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndikukulamula mwamphamvu, pamaso pa Mulungu ndi Khristu Yesu ndiponso angelo ochita kusankhidwa, kuti uzitsatira malangizo amenewa popanda tsankho kapena kukondera.+
21 Ndikukulamula mwamphamvu, pamaso pa Mulungu ndi Khristu Yesu ndiponso angelo ochita kusankhidwa, kuti uzitsatira malangizo amenewa popanda tsankho kapena kukondera.+