1 Timoteyo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usafulumire kuika munthu aliyense pa udindo,*+ kapena kugawana ndi anthu ena machimo awo. Pitiriza kukhala ndi khalidwe loyera. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:22 Nsanja ya Olonda,11/1/2015, tsa. 15
22 Usafulumire kuika munthu aliyense pa udindo,*+ kapena kugawana ndi anthu ena machimo awo. Pitiriza kukhala ndi khalidwe loyera.