2 Timoteyo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwakufuna kwa Mulungu, mogwirizana ndi lonjezo la moyo umene tingapeze chifukwa chokhala otsatira a Khristu Yesu,+
1 Ine Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwakufuna kwa Mulungu, mogwirizana ndi lonjezo la moyo umene tingapeze chifukwa chokhala otsatira a Khristu Yesu,+