2 Timoteyo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatipulumutsa ndiponso anatiitana kuti tikhale oyera,+ osati chifukwa cha ntchito zathu, koma chifukwa cha cholinga chake ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Mulungu anatisonyeza kukoma mtimaku kalekale chifukwa cha Khristu Yesu.
9 Iye anatipulumutsa ndiponso anatiitana kuti tikhale oyera,+ osati chifukwa cha ntchito zathu, koma chifukwa cha cholinga chake ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.+ Mulungu anatisonyeza kukoma mtimaku kalekale chifukwa cha Khristu Yesu.