2 Timoteyo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ambuye Yehova* adzamuchitire chifundo pa tsiku lachiweruzo. Iwe ukudziwa bwino za utumiki wonse umene anachita ku Efeso. 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 30-31
18 Ambuye Yehova* adzamuchitire chifundo pa tsiku lachiweruzo. Iwe ukudziwa bwino za utumiki wonse umene anachita ku Efeso.