2 Timoteyo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho iwe mwana wanga,+ pitiriza kupeza mphamvu mʼkukoma mtima kwakukulu kwa Khristu Yesu.