2 Timoteyo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu awa ndi oona: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+