2 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziwakumbutsa zimenezi nthawi zonse. Uziwalangiza* pamaso pa Mulungu, kuti asamakangane pa mawu. Kuchita zimenezi kulibe phindu mʼpangʼono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera. 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2014, tsa. 14
14 Uziwakumbutsa zimenezi nthawi zonse. Uziwalangiza* pamaso pa Mulungu, kuti asamakangane pa mawu. Kuchita zimenezi kulibe phindu mʼpangʼono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera.