2 Timoteyo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe, maziko olimba a Mulungu adakalipo, ndipo ali ndi chidindo cha mawu akuti: “Yehova* amadziwa anthu ake,”+ ndiponso akuti: “Aliyense woitana pa dzina la Yehova*+ aleke kuchita zosalungama.” 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,7/15/2014, ptsa. 8-10, 12-16
19 Komabe, maziko olimba a Mulungu adakalipo, ndipo ali ndi chidindo cha mawu akuti: “Yehova* amadziwa anthu ake,”+ ndiponso akuti: “Aliyense woitana pa dzina la Yehova*+ aleke kuchita zosalungama.”