2 Timoteyo 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso mwina nzeru zingawabwerere nʼkupulumuka mumsampha wa Mdyerekezi, chifukwa wawagwira amoyo pofuna kuti azichita zofuna zake.+ 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:26 Nsanja ya Olonda,8/15/2012, tsa. 20
26 Komanso mwina nzeru zingawabwerere nʼkupulumuka mumsampha wa Mdyerekezi, chifukwa wawagwira amoyo pofuna kuti azichita zofuna zake.+